Ekisodo 32:32, 33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati mukufuna akhululukireni tchimo lawo.+ Koma ngati simukufuna, chonde ndifufuteni mʼbuku lanu limene mwalemba.”+ 33 Komabe Yehova anauza Mose kuti: “Amene wandichimwira ndi amene ndimufufute mʼbuku langa.
32 Ngati mukufuna akhululukireni tchimo lawo.+ Koma ngati simukufuna, chonde ndifufuteni mʼbuku lanu limene mwalemba.”+ 33 Komabe Yehova anauza Mose kuti: “Amene wandichimwira ndi amene ndimufufute mʼbuku langa.