-
Yesaya 45:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Chifukwa cha mtumiki wanga Yakobo ndi Isiraeli wosankhidwa wanga,
Ine ndikukuitana pokutchula dzina lako.
Ndikukupatsa dzina laulemu, ngakhale kuti sukundidziwa.
-