Salimo 111:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ntchito za manja ake zimadziwika ndi choonadi ndiponso chilungamo.+נ [Nun]Malamulo onse amene amapereka ndi odalirika.+ ס [Samekh] 8 Ndi odalirika* nthawi zonse, kuyambira panopa mpaka kalekale.ע [Ayin]Maziko ake ndi choonadi komanso chilungamo.+ Salimo 119:137 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 137 Ndinu wolungama, inu Yehova,+Ndipo zigamulo zanu ndi zachilungamo.+
7 Ntchito za manja ake zimadziwika ndi choonadi ndiponso chilungamo.+נ [Nun]Malamulo onse amene amapereka ndi odalirika.+ ס [Samekh] 8 Ndi odalirika* nthawi zonse, kuyambira panopa mpaka kalekale.ע [Ayin]Maziko ake ndi choonadi komanso chilungamo.+