Deuteronomo 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Zimenezi zidzachitika pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo likadzaterereka,+Chifukwa tsiku la tsoka lawo layandikira,Ndipo zowagwera zifika mofulumira.’ Deuteronomo 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndikanola lupanga langa lonyezimira,Nʼkukonzekeretsa dzanja langa kuti lipereke chiweruzo,+Ndidzabwezera adani anga,+Ndipo ndidzapereka chilango kwa amene amadana nane. Salimo 94:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 94 Inu Yehova, Mulungu amene amabwezera anthu oipa,+Inu Mulungu amene amabwezera anthu oipa, onetsani kuwala kwanu!
35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Zimenezi zidzachitika pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo likadzaterereka,+Chifukwa tsiku la tsoka lawo layandikira,Ndipo zowagwera zifika mofulumira.’
41 Ndikanola lupanga langa lonyezimira,Nʼkukonzekeretsa dzanja langa kuti lipereke chiweruzo,+Ndidzabwezera adani anga,+Ndipo ndidzapereka chilango kwa amene amadana nane.
94 Inu Yehova, Mulungu amene amabwezera anthu oipa,+Inu Mulungu amene amabwezera anthu oipa, onetsani kuwala kwanu!