Yesaya 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taonani, zinthu zimene ndinaneneratu kalekale zachitika,Tsopano ndikulengeza zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+ Yesaya 65:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Taonani! Ndikulenga kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano.+Ndipo zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso,Kapena kuvutitsa maganizo.+
9 Taonani, zinthu zimene ndinaneneratu kalekale zachitika,Tsopano ndikulengeza zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+
17 Taonani! Ndikulenga kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano.+Ndipo zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso,Kapena kuvutitsa maganizo.+