Yesaya 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa Yehova wakukhuthulirani mzimu wa tulo tofa nato.+Iye watseka maso anu, amene ndi aneneri,+Ndipo waphimba mitu yanu, imene ndi anthu amasomphenya.+
10 Chifukwa Yehova wakukhuthulirani mzimu wa tulo tofa nato.+Iye watseka maso anu, amene ndi aneneri,+Ndipo waphimba mitu yanu, imene ndi anthu amasomphenya.+