Yesaya 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Babulo, amene ndi waulemerero kwambiri* kuposa maufumu onse,+Chinthu chokongola chimene Akasidi amachinyadira,+Adzakhala ngati Sodomu ndi Gomora pa nthawi imene Mulungu anawononga mizindayi.+ Yeremiya 50:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, mʼdzikomo simudzakhalanso anthu.+Dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayangʼanitsitsa mwamanthaNdipo adzamuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+
19 Babulo, amene ndi waulemerero kwambiri* kuposa maufumu onse,+Chinthu chokongola chimene Akasidi amachinyadira,+Adzakhala ngati Sodomu ndi Gomora pa nthawi imene Mulungu anawononga mizindayi.+
13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, mʼdzikomo simudzakhalanso anthu.+Dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayangʼanitsitsa mwamanthaNdipo adzamuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+