Yesaya 40:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi iwe sukudziwa? Kodi sunamve? Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi ndi Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angamvetse* nzeru zake.+ Yesaya 59:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Dzanja la Yehova silinafupike moti nʼkulephera kupulumutsa,+Komanso khutu lake silinagonthe* moti nʼkulephera kumva.+
28 Kodi iwe sukudziwa? Kodi sunamve? Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi ndi Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angamvetse* nzeru zake.+
59 Dzanja la Yehova silinafupike moti nʼkulephera kupulumutsa,+Komanso khutu lake silinagonthe* moti nʼkulephera kumva.+