Mateyu 13:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Atafika mʼdera lakwawo+ anayamba kuwaphunzitsa musunagoge wawo, moti anthu anadabwa ndipo ananena kuti: “Kodi munthu ameneyu, nzeru ndi ntchito zamphamvu zoterezi anazitenga kuti?+
54 Atafika mʼdera lakwawo+ anayamba kuwaphunzitsa musunagoge wawo, moti anthu anadabwa ndipo ananena kuti: “Kodi munthu ameneyu, nzeru ndi ntchito zamphamvu zoterezi anazitenga kuti?+