Mateyu 26:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Ndiyeno anayamba kumulavulira kunkhope+ komanso kumumenya nkhonya.+ Ena anamuwomba mbama+ Maliko 14:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Ndipo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope nʼkumamukhoma nkhonya. Iwo ankamuuza kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali apakhoti anamutenga.+ Luka 22:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Tsopano amuna amene anagwira Yesu aja anayamba kumuchitira zachipongwe+ komanso kumumenya.+ Yohane 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atanena zimenezi, mmodzi wa alonda amene anaima chapafupi anamenya Yesu mbama+ nʼkunena kuti: “Ungamuyankhe choncho wansembe wamkulu?”
65 Ndipo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope nʼkumamukhoma nkhonya. Iwo ankamuuza kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali apakhoti anamutenga.+
22 Atanena zimenezi, mmodzi wa alonda amene anaima chapafupi anamenya Yesu mbama+ nʼkunena kuti: “Ungamuyankhe choncho wansembe wamkulu?”