-
Aroma 15:20, 21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Pochita zimenezi ndinatsimikiza mtima kuti ndisalengeze uthenga wabwino kumene anthu ankadziwa kale za Khristu nʼcholinga choti ndisamange pamaziko a munthu wina, 21 koma ndichite mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Amene sanauzidwepo za iye adzamuona, ndipo amene sanamve adzazindikira.”+
-