Yesaya 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,Iwe dzanja la Yehova!+ Dzuka ngati masiku akale, ngati mʼmibadwo yakale. Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,*+Amene unabaya chilombo chamʼnyanja?+
9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,Iwe dzanja la Yehova!+ Dzuka ngati masiku akale, ngati mʼmibadwo yakale. Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,*+Amene unabaya chilombo chamʼnyanja?+