Yesaya 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ulemerero wa Yehova udzaonekera,+Ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+Chifukwa pakamwa pa Yehova panena.” Yohane 12:37, 38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ngakhale kuti anachita zizindikiro zambiri pamaso pawo, iwo sankamukhulupirira, 38 moti mawu a mneneri Yesaya anakwaniritsidwa. Iye anati: “Yehova,* kodi ndi ndani amene wakhulupirira zinthu zimene anamva kwa ife?*+ Ndipo kodi dzanja la Yehova* laonetsedwa kwa ndani?”+
5 Ulemerero wa Yehova udzaonekera,+Ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+Chifukwa pakamwa pa Yehova panena.”
37 Ngakhale kuti anachita zizindikiro zambiri pamaso pawo, iwo sankamukhulupirira, 38 moti mawu a mneneri Yesaya anakwaniritsidwa. Iye anati: “Yehova,* kodi ndi ndani amene wakhulupirira zinthu zimene anamva kwa ife?*+ Ndipo kodi dzanja la Yehova* laonetsedwa kwa ndani?”+