Yesaya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi+ idzaphuka pachitsa cha Jese,+Ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzabereka zipatso. Zekariya 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno udzamuuze kuti,‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Munthu uyu dzina lake ndi Mphukira.+ Adzaphuka pamalo ake ndipo adzamanga kachisi wa Yehova.+
12 Ndiyeno udzamuuze kuti,‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Munthu uyu dzina lake ndi Mphukira.+ Adzaphuka pamalo ake ndipo adzamanga kachisi wa Yehova.+