-
Yesaya 52:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Panali anthu ambiri amene ankamuyangʼana modabwa,
Chifukwa maonekedwe ake anali atasintha kwambiri kuposa a munthu wina aliyense,
Ndipo kukongola kwa thupi lake kunali kutatha, sanalinso wokongola kuposa anthu,
-