Mateyu 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Izi zikufanana ndi zimene Mwana wa munthu anachita. Iye sanabwere kudzatumikiridwa koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuti awombole anthu ambiri.”+ Aroma 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene tinalibe mtengo wogwira,*+ Khristu anafera anthu osalambira Mulungu pa nthawi imene anakonzeratu. Aroma 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Popeza kusamvera kwa munthu mmodziyo kunachititsa kuti ambiri akhale ochimwa,+ kumvera kwa munthu mmodziyu kudzachititsanso kuti ambiri akhale olungama.+
28 Izi zikufanana ndi zimene Mwana wa munthu anachita. Iye sanabwere kudzatumikiridwa koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuti awombole anthu ambiri.”+
6 Pamene tinalibe mtengo wogwira,*+ Khristu anafera anthu osalambira Mulungu pa nthawi imene anakonzeratu.
19 Popeza kusamvera kwa munthu mmodziyo kunachititsa kuti ambiri akhale ochimwa,+ kumvera kwa munthu mmodziyu kudzachititsanso kuti ambiri akhale olungama.+