Yesaya 49:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ana ako amene unabereka ana ena onse atamwalira, adzakuuza kuti,‘Malowa atichepera. Tipezereni malo oti tizikhalamo.’+
20 Ana ako amene unabereka ana ena onse atamwalira, adzakuuza kuti,‘Malowa atichepera. Tipezereni malo oti tizikhalamo.’+