Yesaya 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taonani Ziyoni, mzinda umene timachitiramo zikondwerero zathu.+ Maso anu adzaona kuti Yerusalemu ndi malo okhalamo abata,Tenti imene sidzachotsedwa.+ Zikhomo zake sizidzazulidwaNdipo zingwe zake sizidzadulidwa.
20 Taonani Ziyoni, mzinda umene timachitiramo zikondwerero zathu.+ Maso anu adzaona kuti Yerusalemu ndi malo okhalamo abata,Tenti imene sidzachotsedwa.+ Zikhomo zake sizidzazulidwaNdipo zingwe zake sizidzadulidwa.