Yesaya 61:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mʼmalo mwa manyazi, mudzalandira madalitso ochuluka kuwirikiza kawiri,Ndipo mʼmalo mochita manyazi, mudzafuula mosangalala chifukwa cha gawo lanu. Inde, mudzalandira madalitso owirikiza kawiri mʼdziko lanu,+ Ndipo mudzasangalala mpaka kalekale.+
7 Mʼmalo mwa manyazi, mudzalandira madalitso ochuluka kuwirikiza kawiri,Ndipo mʼmalo mochita manyazi, mudzafuula mosangalala chifukwa cha gawo lanu. Inde, mudzalandira madalitso owirikiza kawiri mʼdziko lanu,+ Ndipo mudzasangalala mpaka kalekale.+