Yesaya 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzachitira chifundo Yakobo+ ndipo adzasankhanso Isiraeli.+ Iye adzachititsa kuti akhazikike* mʼdziko lawo,+ alendo adzagwirizana nawo ndipo adzakhala limodzi ndi nyumba ya Yakobo.+
14 Yehova adzachitira chifundo Yakobo+ ndipo adzasankhanso Isiraeli.+ Iye adzachititsa kuti akhazikike* mʼdziko lawo,+ alendo adzagwirizana nawo ndipo adzakhala limodzi ndi nyumba ya Yakobo.+