Yesaya 55:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tcherani khutu lanu ndipo mubwere kwa ine.+ Mverani ndipo mudzapitiriza kukhala ndi moyo,Ndithu ine ndidzachita nanu pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale+Lokhudza chikondi chokhulupirika chimene ndinalonjeza Davide. Lonjezo limeneli ndi lodalirika.+ Yeremiya 32:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndidzachita nawo pangano+ lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale. Panganoli lidzakhala lakuti sindidzasiya kuwachitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+
3 Tcherani khutu lanu ndipo mubwere kwa ine.+ Mverani ndipo mudzapitiriza kukhala ndi moyo,Ndithu ine ndidzachita nanu pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale+Lokhudza chikondi chokhulupirika chimene ndinalonjeza Davide. Lonjezo limeneli ndi lodalirika.+
40 Ndidzachita nawo pangano+ lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale. Panganoli lidzakhala lakuti sindidzasiya kuwachitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+