Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 51:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,

      Iwe dzanja la Yehova!+

      Dzuka ngati masiku akale, ngati mʼmibadwo yakale.

      Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,*+

      Amene unabaya chilombo chamʼnyanja?+

  • Yesaya 52:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Yehova waika poyera dzanja lake loyera kuti mitundu yonse ione.+

      Ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzaona zimene Mulungu wathu wachita potipulumutsa.*+

  • Yesaya 59:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iye ataona kuti panalibe munthu aliyense woti nʼkuthandizapo,

      Anadabwa kwambiri kuti palibe amene akulowererapo.

      Choncho anapulumutsa anthu* ndi dzanja lake,

      Ndipo chilungamo chake nʼchimene chinamulimbikitsa kuchita zimenezo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena