Salimo 78:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu anachita zodabwitsa pamaso pa makolo awo,+Mʼdziko la Iguputo, mʼdera la Zowani.+ Salimo 105:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,Kumbukirani zozizwitsa zake ndi ziweruzo zimene wapereka,+
5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,Kumbukirani zozizwitsa zake ndi ziweruzo zimene wapereka,+