Yesaya 55:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Funafunani Yehova pa nthawi imene akupezeka.+ Muitaneni adakali pafupi.+ 7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+
6 Funafunani Yehova pa nthawi imene akupezeka.+ Muitaneni adakali pafupi.+ 7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+