Numeri 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aliyense amene wakhudza munthu amene waphedwa ndi lupanga kunja kwa msasa, kapena mtembo, fupa la munthu, kapenanso manda, adzakhala wodetsedwa kwa masiku 7.+
16 Aliyense amene wakhudza munthu amene waphedwa ndi lupanga kunja kwa msasa, kapena mtembo, fupa la munthu, kapenanso manda, adzakhala wodetsedwa kwa masiku 7.+