Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndidzabweretsa lupanga lobwezera chilango pa inu chifukwa chophwanya pangano.+ Mukadzathawira mʼmizinda yanu, ndidzabweretsa matenda pakati panu+ ndipo mudzaperekedwa mʼdzanja la mdani.+

  • Ezekieli 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,+ mitembo ya anthu awo ikadzakhala pakati pa mafano awo onyansa, kuzungulira maguwa awo onse ansembe,+ paphiri lililonse lalitali, pansonga zonse za mapiri, pansi pa mtengo uliwonse waukulu wamasamba obiriwira, ndiponso pansi pa nthambi za mitengo ikuluikulu pamene ankaperekerapo nsembe zonunkhira kuti asangalatse mafano awo onse onyansa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena