Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ Mateyu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Ndidzaika mzimu wanga pa iye+ ndipo anthu a mitundu ina adzawasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni.
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Ndidzaika mzimu wanga pa iye+ ndipo anthu a mitundu ina adzawasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni.