Ekisodo 29:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku ndipo uzichita zimenezi nthawi zonse.+
38 Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku ndipo uzichita zimenezi nthawi zonse.+