2 Mafumu 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho Rabisake anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+ 2 Mafumu 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako Rabisake anaimirira nʼkulankhula mokweza mʼchilankhulo cha Ayuda kuti: “Imvani mawu a mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri.+ 2 Mafumu 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndi mulungu uti pa milungu yonse ya mayiko, amene wapulumutsa dziko lake mʼmanja mwanga, kuti Yehova athe kupulumutsa Yerusalemu mʼmanja mwanga?”’”+
19 Choncho Rabisake anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+
28 Kenako Rabisake anaimirira nʼkulankhula mokweza mʼchilankhulo cha Ayuda kuti: “Imvani mawu a mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri.+
35 Ndi mulungu uti pa milungu yonse ya mayiko, amene wapulumutsa dziko lake mʼmanja mwanga, kuti Yehova athe kupulumutsa Yerusalemu mʼmanja mwanga?”’”+