Levitiko 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gulu la Aisiraeli lizimupatsa+ ana a mbuzi amphongo awiri kuti akhale nsembe yamachimo ndiponso nkhosa yamphongo imodzi kuti ikhale nsembe yopsereza.
5 Gulu la Aisiraeli lizimupatsa+ ana a mbuzi amphongo awiri kuti akhale nsembe yamachimo ndiponso nkhosa yamphongo imodzi kuti ikhale nsembe yopsereza.