Deuteronomo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu. Musamadzichekecheke+ kapena kumeta nsidze zanu* chifukwa cha anthu akufa.+
14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu. Musamadzichekecheke+ kapena kumeta nsidze zanu* chifukwa cha anthu akufa.+