2 Samueli 7:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhalapobe mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 17 Natani anauza Davide mawu onsewa ndiponso masomphenya onse amene anaona.+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhalapobe mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 17 Natani anauza Davide mawu onsewa ndiponso masomphenya onse amene anaona.+