Deuteronomo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo anthu ochepa okha pakati panu ndi amene adzapulumuke+ mʼmayiko a mitundu imene Yehova adzakuthamangitsireni. Deuteronomo 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mukamakwapula mitengo ya maolivi pokolola, musamabwereze kukwapula nthambi zimene mwakwapula kale. Zimene zatsala zizikhala za mlendo wokhala mʼdziko lanu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.+
27 Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo anthu ochepa okha pakati panu ndi amene adzapulumuke+ mʼmayiko a mitundu imene Yehova adzakuthamangitsireni.
20 Mukamakwapula mitengo ya maolivi pokolola, musamabwereze kukwapula nthambi zimene mwakwapula kale. Zimene zatsala zizikhala za mlendo wokhala mʼdziko lanu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.+