Hoseya 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakati pa anthu a mtundu wanu padzakhala chisokonezo.Ndipo mizinda yanu yonse yokhala ndi mipanda yolimba idzawonongedwa,+Ngati mmene Salimani anawonongera Beti-aribeliPa tsiku lankhondo, pamene azimayi ndi ana awo anawanyenyanyenya. Amosi 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,‘Mdani adzazungulira dziko lonse,+Ameneyo adzakufoola,Ndipo adzatenga zinthu munsanja zako zolimba.’+
14 Pakati pa anthu a mtundu wanu padzakhala chisokonezo.Ndipo mizinda yanu yonse yokhala ndi mipanda yolimba idzawonongedwa,+Ngati mmene Salimani anawonongera Beti-aribeliPa tsiku lankhondo, pamene azimayi ndi ana awo anawanyenyanyenya.
11 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,‘Mdani adzazungulira dziko lonse,+Ameneyo adzakufoola,Ndipo adzatenga zinthu munsanja zako zolimba.’+