Salimo 50:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ganizirani zinthu zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani. Hoseya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Isiraeli anaiwala amene anamupanga+ ndipo wamanga akachisi.+Yuda nayenso wamanga mizinda yambiri yokhala ndi mipanda yolimba.+ Koma ine ndidzatumiza moto mʼmizinda yakeNdipo udzawotcha nsanja zamumzinda uliwonse.”+
22 Ganizirani zinthu zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.
14 Isiraeli anaiwala amene anamupanga+ ndipo wamanga akachisi.+Yuda nayenso wamanga mizinda yambiri yokhala ndi mipanda yolimba.+ Koma ine ndidzatumiza moto mʼmizinda yakeNdipo udzawotcha nsanja zamumzinda uliwonse.”+