Yeremiya 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+ Yeremiya 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako ndinamwetsanso Farao mfumu ya Iguputo, atumiki ake, akalonga ake ndi anthu ake onse+ Ezekieli 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana kwa Farao mfumu ya Iguputo ndipo ulosere zoipa zimene zidzachitikire iyeyo ndi dziko lonse la Iguputo.+ Yoweli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Iguputo adzasanduka bwinja,+Ndipo Edomu adzakhala chipululu chopanda kanthu.+Chifukwa cha nkhanza zimene anachitira anthu a ku Yuda,+Ndiponso chifukwa chokhetsa magazi a anthu osalakwa mʼdziko la Yudalo.+
17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+
2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana kwa Farao mfumu ya Iguputo ndipo ulosere zoipa zimene zidzachitikire iyeyo ndi dziko lonse la Iguputo.+
19 Koma Iguputo adzasanduka bwinja,+Ndipo Edomu adzakhala chipululu chopanda kanthu.+Chifukwa cha nkhanza zimene anachitira anthu a ku Yuda,+Ndiponso chifukwa chokhetsa magazi a anthu osalakwa mʼdziko la Yudalo.+