Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 8:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndipo atakuuzani kuti: “Funsirani kwa anthu olankhula ndi mizimu kapena anthu olosera zamʼtsogolo, omwe amalira ngati mbalame ndiponso kulankhula motsitsa mawu,” kodi mungavomere? Kodi mtundu uliwonse wa anthu suyenera kufunsira kwa Mulungu wake? Kodi akuyenera kufunsira kwa anthu akufa pofuna kuthandiza anthu amoyo?+

  • Machitidwe 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno pamene tinkapita kumalo opempherera, tinakumana ndi mtsikana wina wantchito wogwidwa ndi mzimu, chiwanda cholosera zamʼtsogolo.+ Iye ankachititsa kuti mabwana ake azipindula kwambiri chifukwa cha zoloserazo.

  • Chivumbulutso 18:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kuwala kwa nyale sikudzaunikanso mwa iwe. Mawu a mkwati ndi a mkwatibwi sadzamvekanso mwa iwe, chifukwa amalonda ako anali anthu apamwamba padziko lapansi, ndiponso mitundu yonse ya anthu inasocheretsedwa ndi zochita zako zamizimu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena