Deuteronomo 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu, si lofanana ndi dziko la Iguputo limene munatulukamo. Kumeneko munkafesa mbewu zanu nʼkumazithirira ndi mapazi* anu ngati kuti mukuthirira dimba la ndiwo zamasamba.
10 Dziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu, si lofanana ndi dziko la Iguputo limene munatulukamo. Kumeneko munkafesa mbewu zanu nʼkumazithirira ndi mapazi* anu ngati kuti mukuthirira dimba la ndiwo zamasamba.