Ekisodo 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Matalalawo anawononga china chilichonse mʼdziko lonse la Iguputo. Anapha anthu komanso nyama ndipo anawononga zomera zonse zamʼmunda. Anagwetsanso mitengo yonse yamʼdzikolo.+ Ekisodo 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pa nthawi imeneyo mbewu za fulakesi* ndi balere zinawonongeka, chifukwa balere anali atakhwima ndipo fulakesi anali atachita maluwa. Miyambo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndayala zofunda zabwino pabedi panga,Nsalu za ku Iguputo zokongola kwambiri.*+
25 Matalalawo anawononga china chilichonse mʼdziko lonse la Iguputo. Anapha anthu komanso nyama ndipo anawononga zomera zonse zamʼmunda. Anagwetsanso mitengo yonse yamʼdzikolo.+
31 Pa nthawi imeneyo mbewu za fulakesi* ndi balere zinawonongeka, chifukwa balere anali atakhwima ndipo fulakesi anali atachita maluwa.