25 Ndimalepheretsa zizindikiro za anthu olankhula zinthu zopanda pake,
Ndipo ndine amene ndimachititsa olosera kuti azichita zinthu ngati anthu opusa.+
Ndine amene ndimasokoneza anthu anzeru
Ndiponso amene ndimachititsa kuti nzeru zawo zikhale zopusa.+