Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mʼmawa kutacha, Farao anavutika kwambiri maganizo. Choncho anaitanitsa ansembe onse amatsenga ndi amuna anzeru onse a mu Iguputo, nʼkuwafotokozera malotowo. Koma palibe amene anatha kumumasulira Farao maloto akewo.

  • 1 Mafumu 4:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Nzeru za Solomo zinaposa nzeru za anthu onse a Kumʼmawa komanso nzeru zonse za ku Iguputo.+

  • Machitidwe 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Choncho Mose anaphunzira nzeru zonse za Aiguputo. Iye ankalankhula mwamphamvu ndiponso ankachita zinthu zazikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena