Yeremiya 46:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Lengezani zimenezi mu Iguputo, muzilengeze ku Migidoli.+ Lengezani zimenezi ku Nofi* ndi ku Tahapanesi.+ Munene kuti, ‘Imani mʼmalo anu ndipo mukhale okonzeka,Chifukwa lupanga lidzawononga anthu onse amene akuzungulirani. Ezekieli 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononganso mafano onyansa* nʼkuthetsa milungu yopanda pake ya ku Nofi.*+ Sipadzapezekanso kalonga* wochokera mʼdziko la Iguputo ndipo ndidzachititsa kuti anthu amʼdzikolo azikhala mwamantha.+
14 “Lengezani zimenezi mu Iguputo, muzilengeze ku Migidoli.+ Lengezani zimenezi ku Nofi* ndi ku Tahapanesi.+ Munene kuti, ‘Imani mʼmalo anu ndipo mukhale okonzeka,Chifukwa lupanga lidzawononga anthu onse amene akuzungulirani.
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononganso mafano onyansa* nʼkuthetsa milungu yopanda pake ya ku Nofi.*+ Sipadzapezekanso kalonga* wochokera mʼdziko la Iguputo ndipo ndidzachititsa kuti anthu amʼdzikolo azikhala mwamantha.+