Zekariya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Pa tsiku limenelo mitundu yambiri ya anthu idzakhala kumbali ya Yehova+ ndipo adzakhala anthu anga. Ine ndidzakhala pakati pako.” Ndipo udzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa iwe.
11 “Pa tsiku limenelo mitundu yambiri ya anthu idzakhala kumbali ya Yehova+ ndipo adzakhala anthu anga. Ine ndidzakhala pakati pako.” Ndipo udzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa iwe.