Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake. Yeremiya 51:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Sankhani* mitundu ya anthu kuti ichite naye nkhondo.Sankhani mafumu a ku Mediya,+ abwanamkubwa ake ndi achiwiri kwa olamulira awo onseKomanso mayiko onse amene iwo amawalamulira. Danieli 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 PERESI, ufumu wanu wagawidwa ndipo waperekedwa kwa Amedi ndi Aperisiya.”+ Danieli 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa.+
11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.
28 Sankhani* mitundu ya anthu kuti ichite naye nkhondo.Sankhani mafumu a ku Mediya,+ abwanamkubwa ake ndi achiwiri kwa olamulira awo onseKomanso mayiko onse amene iwo amawalamulira.