Salimo 137:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 137 Tinakhala pansi mʼmphepete mwa mitsinje ya ku Babulo.+ Tinalira titakumbukira Ziyoni.+ Yesaya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 mudzanena mwambi uwu wonyoza mfumu ya Babulo: “Amene ankagwiritsa ntchito anzake mokakamiza uja wawonongedwa! Kuponderezedwa kuja kwatha ndithu!+ Yesaya 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano dziko lonse lapansi lapuma, palibenso chosokoneza. Anthu akufuula mosangalala.+ Yesaya 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu amene Yehova anawawombola adzabwerera+ ndipo adzafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Chisangalalo chosatha chidzakhala ngati chisoti chachifumu kumutu kwawo.+ Adzakhala okondwa ndi osangalalaNdipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+
4 mudzanena mwambi uwu wonyoza mfumu ya Babulo: “Amene ankagwiritsa ntchito anzake mokakamiza uja wawonongedwa! Kuponderezedwa kuja kwatha ndithu!+
10 Anthu amene Yehova anawawombola adzabwerera+ ndipo adzafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Chisangalalo chosatha chidzakhala ngati chisoti chachifumu kumutu kwawo.+ Adzakhala okondwa ndi osangalalaNdipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+