Habakuku 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nditamva mawu ake, mʼmimba mwanga munabwadamuka.Ndipo milomo yanga inanjenjemera. Mafupa anga anayamba kuwola,+Ndipo miyendo yanga inanjenjemera. Koma ndikuyembekezera mofatsa tsiku la masautso.+Chifukwa likubwera kwa anthu amene amatiukira.
16 Nditamva mawu ake, mʼmimba mwanga munabwadamuka.Ndipo milomo yanga inanjenjemera. Mafupa anga anayamba kuwola,+Ndipo miyendo yanga inanjenjemera. Koma ndikuyembekezera mofatsa tsiku la masautso.+Chifukwa likubwera kwa anthu amene amatiukira.