Genesis 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Yakobo anatuma anthu kuti apite kwa mchimwene wake Esau, kudziko la Seiri,+ mʼdera la Edomu.+ Deuteronomo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho tinadutsa pafupi ndi abale athu, mbadwa za Esau,+ amene akukhala ku Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba, Elati ndi Ezioni-geberi.+ Kenako tinatembenuka nʼkudutsa njira ya mʼchipululu cha Mowabu.+ Salimo 137:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, kumbukiraniZimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa. Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+
3 Ndiyeno Yakobo anatuma anthu kuti apite kwa mchimwene wake Esau, kudziko la Seiri,+ mʼdera la Edomu.+
8 Choncho tinadutsa pafupi ndi abale athu, mbadwa za Esau,+ amene akukhala ku Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba, Elati ndi Ezioni-geberi.+ Kenako tinatembenuka nʼkudutsa njira ya mʼchipululu cha Mowabu.+
7 Inu Yehova, kumbukiraniZimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa. Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+