Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 19:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno anawalamula kuti: “Muzichita zotsatirazi moopa Yehova, mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse. 10 Abale anu, amene akukhala mʼmizinda yawo, akabwera ndi mlandu wokhudza kukhetsa magazi+ komanso funso lokhudza malamulo kapena ziweruzo, muziwachenjeza kuti asalakwire Yehova kuopera kuti Mulungu angakukwiyireni kwambiri inuyo ndiponso abale anuwo. Muzichita zimenezi nʼcholinga choti musapalamule mlandu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena