Genesis 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kanani anabereka Sidoni,+ mwana wake woyamba, kenako anabereka Heti.+ Ezekieli 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu a ku Sidoni ndi ku Arivadi+ ndi amene ankakupalasa. Iwe Turo, akatswiri ako odziwa kuyendetsa sitima zapamadzi ndi amene ankakuyendetsa.+
8 Anthu a ku Sidoni ndi ku Arivadi+ ndi amene ankakupalasa. Iwe Turo, akatswiri ako odziwa kuyendetsa sitima zapamadzi ndi amene ankakuyendetsa.+