Ezekieli 27:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu onse amene akukhala mʼzilumba adzakuyangʼanitsitsa modabwa,+Ndipo mafumu awo adzanjenjemera chifukwa cha mantha.+ Nkhope zawo zidzaoneka zankhawa. Ezekieli 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Onse amene ankakudziwa pakati pa mitundu ya anthu adzakuyangʼanitsitsa modabwa.+ Mapeto ako adzakhala odzidzimutsa komanso oopsa,Ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.”’”+
35 Anthu onse amene akukhala mʼzilumba adzakuyangʼanitsitsa modabwa,+Ndipo mafumu awo adzanjenjemera chifukwa cha mantha.+ Nkhope zawo zidzaoneka zankhawa.
19 Onse amene ankakudziwa pakati pa mitundu ya anthu adzakuyangʼanitsitsa modabwa.+ Mapeto ako adzakhala odzidzimutsa komanso oopsa,Ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.”’”+